Numeri 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amenewa ndiwo malamulo+ ndi zigamulo za Yehova, zimene anapereka kwa ana a Isiraeli kudzera kwa Mose ku Yeriko, m’chipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano.+
13 Amenewa ndiwo malamulo+ ndi zigamulo za Yehova, zimene anapereka kwa ana a Isiraeli kudzera kwa Mose ku Yeriko, m’chipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano.+