Numeri 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Mose ndi wansembe Eleazara+ analankhula ndi Aisiraeliwo m’chipululu cha Mowabu,+ pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, kufupi ndi Yeriko,+ kuti: Numeri 33:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Ndipo Yehova analankhula ndi Mose ku Yeriko, pafupi ndi Yorodano, m’chipululu cha Mowabu.+ Anamuuza kuti: Numeri 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yehova analankhula ndi Mose m’chipululu cha Mowabu ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano,+ kuti:
3 Chotero Mose ndi wansembe Eleazara+ analankhula ndi Aisiraeliwo m’chipululu cha Mowabu,+ pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, kufupi ndi Yeriko,+ kuti:
50 Ndipo Yehova analankhula ndi Mose ku Yeriko, pafupi ndi Yorodano, m’chipululu cha Mowabu.+ Anamuuza kuti:
35 Yehova analankhula ndi Mose m’chipululu cha Mowabu ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano,+ kuti: