Yoswa 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Monga ndakulamula kale,+ ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Usachite mantha kapena kuopa,+ pakuti Yehova Mulungu wako ali nawe kulikonse kumene upiteko.”+ 2 Timoteyo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti Mulungu sanatipatse mzimu wamantha,+ koma wamphamvu,+ wachikondi, ndi woti tiziganiza bwino.+
9 Monga ndakulamula kale,+ ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Usachite mantha kapena kuopa,+ pakuti Yehova Mulungu wako ali nawe kulikonse kumene upiteko.”+
7 Pakuti Mulungu sanatipatse mzimu wamantha,+ koma wamphamvu,+ wachikondi, ndi woti tiziganiza bwino.+