Levitiko 19:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Muzisunga malangizo anga onse ndi zigamulo zanga zonse, ndipo muzizitsatira.+ Ine ndine Yehova.’” 1 Mbiri 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Akamatsatira malamulo anga+ ndi zigamulo zanga+ ndi mtima wonse ngati mmene akuchitira lero, ine ndidzakhazikitsa ufumu wake+ ndipo sudzagwedezeka mpaka kalekale.’
7 Akamatsatira malamulo anga+ ndi zigamulo zanga+ ndi mtima wonse ngati mmene akuchitira lero, ine ndidzakhazikitsa ufumu wake+ ndipo sudzagwedezeka mpaka kalekale.’