Yoswa 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ pakuti ndiwe amene utsogolere anthuwa kuti akalandire dziko+ limene ndinalumbirira makolo awo kuti ndidzawapatsa.+ 2 Akorinto 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero nthawi zonse timakhala olimba mtima ndipo tikudziwa kuti pamene tikukhala m’thupi, tili kutali ndi Ambuye,+
6 Ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ pakuti ndiwe amene utsogolere anthuwa kuti akalandire dziko+ limene ndinalumbirira makolo awo kuti ndidzawapatsa.+
6 Chotero nthawi zonse timakhala olimba mtima ndipo tikudziwa kuti pamene tikukhala m’thupi, tili kutali ndi Ambuye,+