Yohane 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiponso, ndikapita kukakukonzerani malo, ndidzabweranso+ kudzakutengerani kwathu,+ kuti kumene kuli ineko inunso mukakhale kumeneko.+
3 Ndiponso, ndikapita kukakukonzerani malo, ndidzabweranso+ kudzakutengerani kwathu,+ kuti kumene kuli ineko inunso mukakhale kumeneko.+