Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 29:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsopano mfumu Davide inauza mpingo wonse+ kuti: “Solomo mwana wanga, amene Mulungu wamusankha,+ ndi wamng’ono+ ndi wosakhwima. Koma ntchitoyi ndi yaikulu chifukwa chinyumba chachikuluchi, si cha munthu ayi,+ koma ndi cha Yehova Mulungu.

  • Yeremiya 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma ine ndinati: “Haa! Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ine sindingathe kulankhula+ chifukwa ndine mwana.”+

  • Mateyu 23:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Aliyense wodzikweza adzatsitsidwa,+ koma aliyense wodzichepetsa adzakwezedwa.+

  • 2 Akorinto 12:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 koma anandiuza motsimikiza kuti: “Kukoma mtima kwakukulu kumene ndakusonyeza n’kokukwanira,+ pakuti mphamvu yanga imakhala yokwanira iweyo ukakhala wofooka.”+ Choncho, ndidzadzitamandira mosangalala kwambiri pa kufooka kwanga,+ kuti mphamvu ya Khristu ikhalebe pamutu panga ngati hema.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena