Deuteronomo 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo Yehova anapitiriza kundikwiyira chifukwa cha inu,+ ndipo sanandimvere. Motero Yehova anandiuza kuti, ‘Basi khala chete! Usatchulenso nkhani imeneyi kwa ine.
26 Pamenepo Yehova anapitiriza kundikwiyira chifukwa cha inu,+ ndipo sanandimvere. Motero Yehova anandiuza kuti, ‘Basi khala chete! Usatchulenso nkhani imeneyi kwa ine.