Yesaya 40:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye amapereka mphamvu kwa munthu wotopa,+ ndipo wofooka amam’patsa nyonga zochuluka.+ Aheberi 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Anagonjetsa mphamvu ya moto,+ anathawa lupanga,+ anali ofooka koma anapatsidwa mphamvu,+ analimba mtima pa nkhondo,+ ndiponso anagonjetsa magulu ankhondo a mayiko ena.+
34 Anagonjetsa mphamvu ya moto,+ anathawa lupanga,+ anali ofooka koma anapatsidwa mphamvu,+ analimba mtima pa nkhondo,+ ndiponso anagonjetsa magulu ankhondo a mayiko ena.+