2 Samueli 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Davide anayamba kutonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kuwonjezera apo, analowa kwa iye ndipo anagona naye. Patapita nthawi, anamuberekera mwana wamwamuna+ amene anamutcha dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anam’konda mwana ameneyu.+ 1 Mafumu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zomwe zidzachitike n’zoti, inuyo mbuyanga mfumu mukadzangogona m’manda limodzi ndi makolo anu,+ ineyo ndi mwana wanga Solomo tidzaoneka ngati olakwa.”
24 Ndiyeno Davide anayamba kutonthoza mkazi wake Bati-seba.+ Kuwonjezera apo, analowa kwa iye ndipo anagona naye. Patapita nthawi, anamuberekera mwana wamwamuna+ amene anamutcha dzina lakuti Solomo.*+ Yehova anam’konda mwana ameneyu.+
21 Zomwe zidzachitike n’zoti, inuyo mbuyanga mfumu mukadzangogona m’manda limodzi ndi makolo anu,+ ineyo ndi mwana wanga Solomo tidzaoneka ngati olakwa.”