1 Mbiri 29:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero, Solomo anayamba kukhala pampando wachifumu wa Yehova+ monga mfumu m’malo mwa Davide bambo wake, ndipo ankalamulira bwino.+ Aisiraeli onse anali kumumvera. 2 Mbiri 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Solomo atamva zimenezi anauza Mulungu kuti: “Inu ndinu amene mwasonyeza kukoma mtima kosatha kwa Davide bambo anga,+ ndipo mwandiika kukhala mfumu m’malo mwake.+
23 Chotero, Solomo anayamba kukhala pampando wachifumu wa Yehova+ monga mfumu m’malo mwa Davide bambo wake, ndipo ankalamulira bwino.+ Aisiraeli onse anali kumumvera.
8 Solomo atamva zimenezi anauza Mulungu kuti: “Inu ndinu amene mwasonyeza kukoma mtima kosatha kwa Davide bambo anga,+ ndipo mwandiika kukhala mfumu m’malo mwake.+