1 Mbiri 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Tsopano mwana wanga, Yehova akhale nawe, ndipo zinthu zikuyendere bwino kuti umange nyumba ya Yehova Mulungu wako, monga mmene iye analankhulira za iwe.+
11 “Tsopano mwana wanga, Yehova akhale nawe, ndipo zinthu zikuyendere bwino kuti umange nyumba ya Yehova Mulungu wako, monga mmene iye analankhulira za iwe.+