1 Mafumu 1:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Solomo atamva anati: “Akadzakhala munthu wolimba mtima, ngakhale tsitsi lake limodzi+ silidzathothoka n’kugwera pansi, koma choipa chikadzapezeka mwa iye,+ adzaphedwa.”+ Mlaliki 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Popeza anthu ochita zoipa sanalangidwe msanga,+ n’chifukwa chake mtima wa ana a anthu wakhazikika pa kuchita zoipa.+
52 Solomo atamva anati: “Akadzakhala munthu wolimba mtima, ngakhale tsitsi lake limodzi+ silidzathothoka n’kugwera pansi, koma choipa chikadzapezeka mwa iye,+ adzaphedwa.”+
11 Popeza anthu ochita zoipa sanalangidwe msanga,+ n’chifukwa chake mtima wa ana a anthu wakhazikika pa kuchita zoipa.+