Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Musamakondere poweruza.+ Munthu wamba ndi munthu wolemekezeka onse muziwamvetsera chimodzimodzi.+ Musamaope munthu+ chifukwa mukuweruzira Mulungu.+ Mlandu umene wakuvutani muziubweretsa kwa ine kuti ndiumve.’+

  • 1 Mafumu 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mfumu Solomo itatero, inalumbira pamaso pa Yehova kuti: “Mulungu andilange mowirikiza+ ngati Adoniya sanaike moyo wake pangozi mwa kupempha zimenezi.+

  • Miyambo 13:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Chilungamo chimateteza munthu amene sachita zopweteka ena,+ koma wochimwa amawonongedwa ndi zoipa.+

  • Miyambo 21:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mulungu wolungama amayang’ana nyumba ya munthu woipa,+ ndipo anthu oipa amawagwetsa kuti akumane ndi tsoka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena