Salimo 64:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo iwo amakhumudwitsa munthu,+Koma lilime lawo likutsutsana nawo.+Onse owayang’ana adzapukusa mitu yawo,+ Salimo 140:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kunena za anthu amene andizungulira,+Zoipa zotuluka pakamwa pawo ziphimbe mitu yawo.+
8 Ndipo iwo amakhumudwitsa munthu,+Koma lilime lawo likutsutsana nawo.+Onse owayang’ana adzapukusa mitu yawo,+ Salimo 140:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kunena za anthu amene andizungulira,+Zoipa zotuluka pakamwa pawo ziphimbe mitu yawo.+