Yeremiya 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho dziko lawo lidzakhala chinthu chodabwitsa kwa ena,+ chinthu chimene adzachiimbira mluzu mpaka kalekale.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi dzikoli adzaliyang’anitsitsa modabwa ndipo adzapukusa mutu wake.+ Chivumbulutso 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo ataima patali poona kuzunzika kwake, adzati,+ ‘Kalanga ine! Kalanga ine! Mzinda waukuluwe!+ Babulo iwe, mzinda wamphamvu! Chifukwa mu ola limodzi, chiweruzo chako chafika!’+
16 Choncho dziko lawo lidzakhala chinthu chodabwitsa kwa ena,+ chinthu chimene adzachiimbira mluzu mpaka kalekale.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi dzikoli adzaliyang’anitsitsa modabwa ndipo adzapukusa mutu wake.+
10 Ndipo ataima patali poona kuzunzika kwake, adzati,+ ‘Kalanga ine! Kalanga ine! Mzinda waukuluwe!+ Babulo iwe, mzinda wamphamvu! Chifukwa mu ola limodzi, chiweruzo chako chafika!’+