Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukupitikitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja,+ ndipo mizinda yanu idzawonongedwa ndi kukhala mabwinja.

  • Yeremiya 19:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndidzasandutsa mzindawu kukhala chinthu chodabwitsa kwa ena, chimene azidzachiimbira mluzu.+ Aliyense wodutsa pafupi nawo adzauyang’anitsitsa modabwa ndipo adzaulizira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+

  • Yeremiya 49:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Ine ndalumbira pa dzina langa+ kuti Bozira+ adzakhala chinthu chodabwitsa, chotonzedwa ndiponso malo owonongedwa.+ Iye adzakhala wotembereredwa ndipo mizinda yake yonse idzakhala mabwinja mpaka kalekale,”+ watero Yehova.

  • Ezekieli 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndidzawatambasulira dzanja langa powalanga+ ndipo dziko lawo ndidzalisandutsa bwinja. Malo awo onse okhala adzakhala bwinja loipa kuposa chipululu cha Dibula, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena