-
Ezekieli 6:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndidzatambasula dzanja langa nʼkuwalanga ndipo dziko lawo ndidzalisandutsa bwinja. Malo awo onse amene amakhala adzasanduka bwinja loipa kwambiri kuposa chipululu chimene chili pafupi ndi Dibula. Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”
-