Ezekieli 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzawatambasulira dzanja langa powalanga+ ndipo dziko lawo ndidzalisandutsa bwinja. Malo awo onse okhala adzakhala bwinja loipa kuposa chipululu cha Dibula, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’” Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:14 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 13
14 Ndidzawatambasulira dzanja langa powalanga+ ndipo dziko lawo ndidzalisandutsa bwinja. Malo awo onse okhala adzakhala bwinja loipa kuposa chipululu cha Dibula, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”