Yeremiya 51:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Babulo wagwa mwadzidzidzi moti wasweka.+ Mulireni mofuula anthu inu.+ M’patseni mafuta a basamu kuti muthetse ululu wake,+ mwina achira.”
8 Babulo wagwa mwadzidzidzi moti wasweka.+ Mulireni mofuula anthu inu.+ M’patseni mafuta a basamu kuti muthetse ululu wake,+ mwina achira.”