Yeremiya 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anthu a ku Mowabu achita manyazi pakuti agwidwa ndi mantha aakulu.+ Lirani mofuula. Amuna inu, lengezani ku Arinoni+ kuti Mowabu wafunkhidwa. Chivumbulutso 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Mafumu+ a dziko lapansi amene anachita naye dama ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa ndi chisoni chifukwa cha iye,+ poona utsi+ wofuka chifukwa cha kupsa kwake.
20 Anthu a ku Mowabu achita manyazi pakuti agwidwa ndi mantha aakulu.+ Lirani mofuula. Amuna inu, lengezani ku Arinoni+ kuti Mowabu wafunkhidwa.
9 “Mafumu+ a dziko lapansi amene anachita naye dama ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa ndi chisoni chifukwa cha iye,+ poona utsi+ wofuka chifukwa cha kupsa kwake.