Yeremiya 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mowabu wachititsidwa manyazi ndipo wagwidwa ndi mantha aakulu. Lirani mofuula. Lengezani ku Arinoni+ kuti Mowabu wawonongedwa.
20 Mowabu wachititsidwa manyazi ndipo wagwidwa ndi mantha aakulu. Lirani mofuula. Lengezani ku Arinoni+ kuti Mowabu wawonongedwa.