Yeremiya 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anthu a ku Mowabu achita manyazi pakuti agwidwa ndi mantha aakulu.+ Lirani mofuula. Amuna inu, lengezani ku Arinoni+ kuti Mowabu wafunkhidwa.
20 Anthu a ku Mowabu achita manyazi pakuti agwidwa ndi mantha aakulu.+ Lirani mofuula. Amuna inu, lengezani ku Arinoni+ kuti Mowabu wafunkhidwa.