Yeremiya 51:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Babulo wagwa mwadzidzidzi ndipo wasweka.+ Mulirireni mofuula.+ Mʼpatseni mafuta a basamu kuti ululu wake uthe, mwina angachire.” Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:8 Nsanja ya Olonda,1/15/2002, ptsa. 30-31
8 Babulo wagwa mwadzidzidzi ndipo wasweka.+ Mulirireni mofuula.+ Mʼpatseni mafuta a basamu kuti ululu wake uthe, mwina angachire.”