Yesaya 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Taonani zimene zikubwera: Kukubwera amuna amene akwera galeta lankhondo limene likukokedwa ndi mahatchi awiri.”+ Kenako iye analankhula kuti: “Wagwa! Babulo wagwa!+ Zifaniziro zonse zogoba za milungu yake zaphwanyidwa ndipo zili pansi.”+ Yesaya 47:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma zinthu ziwiri izi zidzakugwera modzidzimutsa tsiku limodzi:+ Ana ako adzafa ndiponso udzakhala wamasiye. Zinthu zonsezi zidzakugwera ndithu,+Chifukwa* wachita zanyanga zochuluka komanso chifukwa cha zamatsenga zako zonse zamphamvu.+ Chivumbulutso 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako mngelo wachiwiri anamutsatira ndipo anati: “Wagwa! Babulo Wamkulu+ wagwa,+ amene anachititsa kuti mitundu yonse ya anthu imwe vinyo wa chilakolako cha* chiwerewere* chake!”+
9 Taonani zimene zikubwera: Kukubwera amuna amene akwera galeta lankhondo limene likukokedwa ndi mahatchi awiri.”+ Kenako iye analankhula kuti: “Wagwa! Babulo wagwa!+ Zifaniziro zonse zogoba za milungu yake zaphwanyidwa ndipo zili pansi.”+
9 Koma zinthu ziwiri izi zidzakugwera modzidzimutsa tsiku limodzi:+ Ana ako adzafa ndiponso udzakhala wamasiye. Zinthu zonsezi zidzakugwera ndithu,+Chifukwa* wachita zanyanga zochuluka komanso chifukwa cha zamatsenga zako zonse zamphamvu.+
8 Kenako mngelo wachiwiri anamutsatira ndipo anati: “Wagwa! Babulo Wamkulu+ wagwa,+ amene anachititsa kuti mitundu yonse ya anthu imwe vinyo wa chilakolako cha* chiwerewere* chake!”+