Yesaya 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano taonani! Kukubwera magaleta ankhondo okokedwa ndi mahatchi awiriawiri, mutakwera amuna ankhondo.”+ Kenako iye anayamba kufuula kuti: “Wagwa! Babulo wagwa!+ Zifaniziro zonse zogoba za milungu yake zaphwanyidwa ndipo zili pansi.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:9 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 260 Nsanja ya Olonda,1/1/2000, ptsa. 7-8 Yesaya 1, ptsa. 223-224
9 Tsopano taonani! Kukubwera magaleta ankhondo okokedwa ndi mahatchi awiriawiri, mutakwera amuna ankhondo.”+ Kenako iye anayamba kufuula kuti: “Wagwa! Babulo wagwa!+ Zifaniziro zonse zogoba za milungu yake zaphwanyidwa ndipo zili pansi.”+