Esitere 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anapachika Hamani pamtengo+ umene anakonzera Moredekai,+ ndipo mkwiyo wa mfumu unatha. Salimo 94:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye adzawabwezera zoipa zawo,+Ndipo adzawakhalitsa chete mwa kuwadzetsera masoka okonza okha.+Yehova Mulungu wathu adzawakhalitsa chete.+ Miyambo 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu woipa amakodwa ndi kuchimwa kwa milomo yake,+ koma wolungama amachoka m’masautso.+ Miyambo 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakamwa pa munthu wopusa m’pamene pamamuwononga,+ ndipo milomo yake ndi msampha wa moyo wake.+
23 Iye adzawabwezera zoipa zawo,+Ndipo adzawakhalitsa chete mwa kuwadzetsera masoka okonza okha.+Yehova Mulungu wathu adzawakhalitsa chete.+