Miyambo 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munthu wanzeru mumtima mwake amamvera malamulo,+ koma wamilomo yopusa amaponderezedwa.+ Miyambo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anzeru ndiwo amapitiriza kuphunzira zinthu zamtengo wapatali,+ koma pakamwa pa wopusa patsala pang’ono kuwonongeka.+ Miyambo 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene amayang’anira pakamwa pake amasunga moyo wake.+ Amene amatsegula kwambiri pakamwa pake adzawonongeka.+ Mlaliki 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mawu a m’kamwa mwa munthu wanzeru amakhala osangalatsa,+ koma milomo ya munthu wopusa imamuwononga.+
14 Anzeru ndiwo amapitiriza kuphunzira zinthu zamtengo wapatali,+ koma pakamwa pa wopusa patsala pang’ono kuwonongeka.+
3 Amene amayang’anira pakamwa pake amasunga moyo wake.+ Amene amatsegula kwambiri pakamwa pake adzawonongeka.+
12 Mawu a m’kamwa mwa munthu wanzeru amakhala osangalatsa,+ koma milomo ya munthu wopusa imamuwononga.+