Salimo 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+ Salimo 141:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, ikani mlonda pakamwa panga.+Ikani wolondera patsogolo pa milomo yanga.+ Miyambo 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Wosunga pakamwa pake ndiponso lilime lake akuteteza moyo wake ku masautso.+
39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+