Miyambo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pereka malangizo kwa munthu wanzeru ndipo adzawonjezera nzeru zake.+ Phunzitsa munthu wolungama ndipo adzapitiriza kuphunzira. Miyambo 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mtima wa munthu womvetsa zinthu umadziwa zinthu,+ ndipo khutu la anzeru limafunafuna kudziwa zinthu.+ Mateyu 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chake chabwino,+ koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa.+
9 Pereka malangizo kwa munthu wanzeru ndipo adzawonjezera nzeru zake.+ Phunzitsa munthu wolungama ndipo adzapitiriza kuphunzira.
15 Mtima wa munthu womvetsa zinthu umadziwa zinthu,+ ndipo khutu la anzeru limafunafuna kudziwa zinthu.+
35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chake chabwino,+ koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa.+