1 Mafumu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mupatse mtumiki wanune mtima womvera kuti ndiweruze+ anthu anu, ndi kusiyanitsa pakati pa chabwino ndi choipa,+ pakuti ndani angathe kuweruza+ anthu anu ovutawa?”+ Miyambo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pereka malangizo kwa munthu wanzeru ndipo adzawonjezera nzeru zake.+ Phunzitsa munthu wolungama ndipo adzapitiriza kuphunzira. Miyambo 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mtima womvetsa ndi umene umafunafuna kudziwa zinthu,+ koma pakamwa pa anthu opusa m’pamene pamafunafuna kulankhula zopusa.+
9 Mupatse mtumiki wanune mtima womvera kuti ndiweruze+ anthu anu, ndi kusiyanitsa pakati pa chabwino ndi choipa,+ pakuti ndani angathe kuweruza+ anthu anu ovutawa?”+
9 Pereka malangizo kwa munthu wanzeru ndipo adzawonjezera nzeru zake.+ Phunzitsa munthu wolungama ndipo adzapitiriza kuphunzira.
14 Mtima womvetsa ndi umene umafunafuna kudziwa zinthu,+ koma pakamwa pa anthu opusa m’pamene pamafunafuna kulankhula zopusa.+