Miyambo 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Munthu wochenjera amabisa zimene akudziwa,+ koma mtima wa anthu opusa umalengeza zopusa.+ Yesaya 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+ Hoseya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Efuraimu akudya mphepo+ ndi kuthamangitsa mphepo ya kum’mawa tsiku lonse.+ Iye akuchulukitsa mabodza ndipo akuwononga zinthu zambiri.+ Wachita pangano ndi Asuri+ ndipo wapititsa mafuta ku Iguputo.
10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+
12 “Efuraimu akudya mphepo+ ndi kuthamangitsa mphepo ya kum’mawa tsiku lonse.+ Iye akuchulukitsa mabodza ndipo akuwononga zinthu zambiri.+ Wachita pangano ndi Asuri+ ndipo wapititsa mafuta ku Iguputo.