Hoseya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Efuraimu akudya mphepo. Akuthamangitsa mphepo yakumʼmawa tsiku lonse. Iye akuchulukitsa mabodza ndi chiwawa. Wachita pangano ndi Asuri+ ndipo wapititsa mafuta ku Iguputo.+
12 “Efuraimu akudya mphepo. Akuthamangitsa mphepo yakumʼmawa tsiku lonse. Iye akuchulukitsa mabodza ndi chiwawa. Wachita pangano ndi Asuri+ ndipo wapititsa mafuta ku Iguputo.+