2 Mafumu 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Puli+ mfumu ya Asuri anabwera mʼdzikomo ndipo Menahemu anamupatsa matalente* 1,000 a siliva chifukwa choti anamuthandiza kulimbitsa ufumu.+ Hoseya 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo akafika mpaka kudziko la Asuri+ ngati bulu wamʼtchire. Efuraimu walipira akazi kuti azigona nawo.+
19 Puli+ mfumu ya Asuri anabwera mʼdzikomo ndipo Menahemu anamupatsa matalente* 1,000 a siliva chifukwa choti anamuthandiza kulimbitsa ufumu.+
9 Iwo akafika mpaka kudziko la Asuri+ ngati bulu wamʼtchire. Efuraimu walipira akazi kuti azigona nawo.+