2 Mafumu 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano Puli+ mfumu ya Asuri+ inabwera m’dzikomo. Choncho Menahemu anapatsa+ Puli matalente* 1,000 a siliva,+ kuti amuthandize kulimbitsa ufumu umene unali m’manja mwake.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:19 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 26
19 Tsopano Puli+ mfumu ya Asuri+ inabwera m’dzikomo. Choncho Menahemu anapatsa+ Puli matalente* 1,000 a siliva,+ kuti amuthandize kulimbitsa ufumu umene unali m’manja mwake.+