Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 “Matemberero onsewa+ adzakugwera, kukutsatira ndi kukupeza kufikira utafafanizika,+ chifukwa sunamvere mawu a Yehova Mulungu wako mwa kusunga malamulo ndi mfundo zake zimene anakupatsa.+

  • 2 Mafumu 12:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pamenepo Yehoasi mfumu ya Yuda anatenga zopereka zonse zopatulika+ zimene Yehosafati, Yehoramu, ndi Ahaziya makolo ake, mafumu a Yuda anaziyeretsa. Anatenganso zopereka za iyeyo zopatulika, ndi golide yense yemwe anali mosungira chuma cha m’nyumba ya Yehova ndi cha m’nyumba ya mfumu n’kutumiza+ zonsezi kwa Hazaeli mfumu ya Siriya. Chotero Hazaeli anabwerera osaukira Yerusalemu.

  • 2 Mafumu 16:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pamenepo Ahazi anatenga siliva ndi golide amene anali panyumba ya Yehova+ ndiponso wochokera pa chuma cha m’nyumba ya mfumu, n’kuzitumiza kwa mfumu ya Asuri ngati chiphuphu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena