2 Mafumu 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo Ahazi anatenga siliva ndi golide amene anali panyumba ya Yehova+ ndiponso wochokera pa chuma cha m’nyumba ya mfumu, n’kuzitumiza kwa mfumu ya Asuri ngati chiphuphu.+ 2 Mafumu 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Hezekiya anapereka siliva yense amene anali panyumba ya Yehova,+ ndiponso amene anali pa chuma cha m’nyumba ya mfumu.+
8 Pamenepo Ahazi anatenga siliva ndi golide amene anali panyumba ya Yehova+ ndiponso wochokera pa chuma cha m’nyumba ya mfumu, n’kuzitumiza kwa mfumu ya Asuri ngati chiphuphu.+
15 Ndiyeno Hezekiya anapereka siliva yense amene anali panyumba ya Yehova,+ ndiponso amene anali pa chuma cha m’nyumba ya mfumu.+