Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 15:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Asa ataona zimenezi anatenga siliva ndi golide yense amene anatsala pa chuma cha m’nyumba ya Yehova, ndi pa chuma cha m’nyumba ya mfumu, n’kumupereka kwa atumiki ake. Kenako Mfumu Asa inatumiza atumiki akewo kwa Beni-hadadi+ mwana wa Tabirimoni, mwana wa Hezioni, mfumu ya Siriya,+ amene anali kukhala ku Damasiko.+ Inawatuma kuti akamuuze Beni-hadadi kuti:

  • 2 Mafumu 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yehoasi anatenga golide ndi siliva yense, ndi ziwiya zonse zimene anazipeza panyumba ya Yehova+ ndi m’nyumba yosungiramo chuma cha mfumu. Anagwiranso anthu ena n’kubwerera ku Samariya.

  • 2 Mbiri 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano Asa anatenga siliva ndi golide pa chuma cha m’nyumba ya Yehova+ ndiponso cha m’nyumba ya mfumu,+ n’kuzitumiza kwa Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya+ amene anali kukhala ku Damasiko.+ Anam’tumiziranso mawu akuti:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena