2 Mbiri 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano Asa anatenga siliva ndi golide pa chuma cha m’nyumba ya Yehova+ ndiponso cha m’nyumba ya mfumu,+ n’kuzitumiza kwa Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya+ amene anali kukhala ku Damasiko.+ Anam’tumiziranso mawu akuti:
2 Tsopano Asa anatenga siliva ndi golide pa chuma cha m’nyumba ya Yehova+ ndiponso cha m’nyumba ya mfumu,+ n’kuzitumiza kwa Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya+ amene anali kukhala ku Damasiko.+ Anam’tumiziranso mawu akuti: