-
2 Mafumu 12:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Pamenepo Yehoasi mfumu ya Yuda anatenga zopereka zonse zopatulika+ zimene Yehosafati, Yehoramu, ndi Ahaziya makolo ake, mafumu a Yuda anaziyeretsa. Anatenganso zopereka za iyeyo zopatulika, ndi golide yense yemwe anali mosungira chuma cha m’nyumba ya Yehova ndi cha m’nyumba ya mfumu n’kutumiza+ zonsezi kwa Hazaeli mfumu ya Siriya. Chotero Hazaeli anabwerera osaukira Yerusalemu.
-