1 Mafumu 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mayiyo ataona zimenezi anauza Eliya kuti: “Tsopano ndadziwadi kuti ndinu munthu wa Mulungu+ ndipo mawu a Yehova amene ali m’kamwa mwanu ndi oona.”+
24 Mayiyo ataona zimenezi anauza Eliya kuti: “Tsopano ndadziwadi kuti ndinu munthu wa Mulungu+ ndipo mawu a Yehova amene ali m’kamwa mwanu ndi oona.”+