1 Mafumu 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya anasonkhanitsa gulu lake lonse lankhondo ndiponso mahatchi+ ndi magaleta.+ Atatero ananyamuka pamodzi ndi mafumu ena 32,+ n’kupita kukazungulira+ mzinda wa Samariya+ kuti amenyane nawo. 2 Mafumu 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pambuyo pake Beni-hadadi mfumu ya Siriya anasonkhanitsa asilikali ake onse ndipo anapita kukazungulira+ mzinda wa Samariya.
20 Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya anasonkhanitsa gulu lake lonse lankhondo ndiponso mahatchi+ ndi magaleta.+ Atatero ananyamuka pamodzi ndi mafumu ena 32,+ n’kupita kukazungulira+ mzinda wa Samariya+ kuti amenyane nawo.
24 Pambuyo pake Beni-hadadi mfumu ya Siriya anasonkhanitsa asilikali ake onse ndipo anapita kukazungulira+ mzinda wa Samariya.