24 Davide atapha+ anthu a ku Zoba, Rezoni anayamba kusonkhanitsa anthu kumbali yake, ndipo anakhala mtsogoleri wa gulu la achifwamba. Chotero iye ndi gulu lakelo anapita kukakhala ku Damasiko,+ n’kuyamba kulamulira kumeneko.
5 Ndidzathyola mipiringidzo ya zipata za Damasiko+ ndi kupha anthu a ku Bikati-aveni. Ndidzaphanso munthu wogwira ndodo yachifumu wa ku Beti-edeni, ndipo anthu a ku Siriya adzatengedwa kupita ku ukapolo ku Kiri,”+ watero Yehova.’