2 Samueli 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Asiriyawo anathawa+ pamaso pa Isiraeli, ndipo Davide anapha asilikali a Siriya 700 okwera magaleta,+ ndi asilikali 40,000 okwera pamahatchi. Iye anakanthanso Sobaki, mtsogoleri wa gulu lankhondo la Siriya, moti anafera pomwepo.+
18 Asiriyawo anathawa+ pamaso pa Isiraeli, ndipo Davide anapha asilikali a Siriya 700 okwera magaleta,+ ndi asilikali 40,000 okwera pamahatchi. Iye anakanthanso Sobaki, mtsogoleri wa gulu lankhondo la Siriya, moti anafera pomwepo.+