2 Mafumu 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mfumu ya Asuri inamumvera n’kupita ku Damasiko+ ndipo inakalanda mzindawo.+ Anthu a mumzindawo inawatengera ku Kiri,+ ndipo Rezini+ inamupha. Amosi 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzatumiza moto+ panyumba ya Hazaeli,+ ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za Beni-hadadi.+
9 Mfumu ya Asuri inamumvera n’kupita ku Damasiko+ ndipo inakalanda mzindawo.+ Anthu a mumzindawo inawatengera ku Kiri,+ ndipo Rezini+ inamupha.