1 Mafumu 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Yehova anamuuza kuti: “Nyamuka, bwerera udzere kuchipululu cha Damasiko.+ Pita ukadzoze+ Hazaeli+ kuti akhale mfumu ya Siriya. 2 Mafumu 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mfumuyo itamva zimenezi, inauza Hazaeli kuti:+ “Tenga mphatso,+ upite kukakumana ndi munthu wa Mulungu woonayo. Ukafunsire+ mawu a Yehova kudzera mwa iye kuti, ‘Kodi ndichira matenda angawa?’”
15 Kenako Yehova anamuuza kuti: “Nyamuka, bwerera udzere kuchipululu cha Damasiko.+ Pita ukadzoze+ Hazaeli+ kuti akhale mfumu ya Siriya.
8 Mfumuyo itamva zimenezi, inauza Hazaeli kuti:+ “Tenga mphatso,+ upite kukakumana ndi munthu wa Mulungu woonayo. Ukafunsire+ mawu a Yehova kudzera mwa iye kuti, ‘Kodi ndichira matenda angawa?’”