-
2 Mafumu 8:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Hazaeli ataona zimenezi anafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukulira mbuyanga?” Elisa anayankha kuti: “Chifukwa ndikudziwa bwino zoipa+ zimene iweyo udzachitire ana a Isiraeli. Malo awo otetezedwa udzawatentha ndi moto, amuna ochita kusankhidwa pakati pawo udzawapha ndi lupanga, ana awo aang’ono udzawaphwanyaphwanya,+ ndipo akazi awo apakati udzawatumbula.”+
-