Yeremiya 49:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Mipanda ya Damasiko ndidzaiyatsa moto, ndipo motowo udzatentha nsanja zokhalamo za Beni-hadadi.”+
27 “Mipanda ya Damasiko ndidzaiyatsa moto, ndipo motowo udzatentha nsanja zokhalamo za Beni-hadadi.”+