Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Poyankha mtumikiyo anauzanso Sauli kuti: “Inetu ndili ndi gawo limodzi mwa magawo anayi a sekeli*+ la siliva loti ndingam’patse munthu wa Mulungu woonayo ndipo adzatiuza kumene tingalowere.”

  • 1 Mafumu 14:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Utenge mitanda 10 ya mkate,+ makeke, ndi botolo+ la uchi, ndipo ukafike kwa iyeyo.+ Iye ndiye akakuuze zimene zichitikire mnyamatayu.”+

  • 2 Mafumu 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno mfumu ya Siriya inauza Namani kuti: “Nyamuka, ndikupatsa kalata upite kwa mfumu ya Isiraeli.” Choncho iye ananyamuka atatenga+ matalente* 10 a siliva, masekeli 6,000 a golide,+ ndi zovala 10.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena