Numeri 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero, akuluakulu a ku Mowabu ndi a ku Midiyani anapita kwa Balamu+ atatenga malipiro okamulipira kuti awawombezere maula,+ komanso anamuuza zimene Balaki ananena. 1 Samueli 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Poyankha mtumikiyo anauzanso Sauli kuti: “Inetu ndili ndi gawo limodzi mwa magawo anayi a sekeli*+ la siliva loti ndingam’patse munthu wa Mulungu woonayo ndipo adzatiuza kumene tingalowere.”
7 Chotero, akuluakulu a ku Mowabu ndi a ku Midiyani anapita kwa Balamu+ atatenga malipiro okamulipira kuti awawombezere maula,+ komanso anamuuza zimene Balaki ananena.
8 Poyankha mtumikiyo anauzanso Sauli kuti: “Inetu ndili ndi gawo limodzi mwa magawo anayi a sekeli*+ la siliva loti ndingam’patse munthu wa Mulungu woonayo ndipo adzatiuza kumene tingalowere.”